13.Ndipo Mthenga wa Mulungu anati kwa iwo: “Samalirani ngamira ya ikazi ya Mulungu ndi tsiku lake lomwa madzi!”
14.Iwo sadakhulupirire ayi ndipo ngamirayo adaipha. Motero Ambuye wawo adawaononga chifukwa cha machimo awo ndipo adafafaniza onse mosasankha