4.Angelo ndi Mzimu amakwera kupita kwa Iye mtsiku limodzi limene lingafanizidwe ndi zaka zikwi makumi asanu
11.Iwo azidzawaona iwo. Munthu wochita zoipa adzafunitsitsa kuti mwina akhoza kudzipulumutsa ku chilango cha tsikuli popereka ana ake
42.Motero asiye ayambe adzinyenga ndi chisangalalo mpaka pamene adzakumana ndi tsiku lawo limene adalonjezedwa
43.Tsiku limene adzatuluka mwansanga m’manda mwawo ngati anthu a pa mpikisano umene amalandirirapo mphotho
44.Atayang’ana maso awo pansi ndipo adzachititsidwa manyazi. Limeneli ndilo tsiku limene analonjezedwa