الحاج یوسف محمد کنیمولا · chiCheŵa, chinyanja

1.Oh iwe Mtumwi! Bwanji ukudziletsa zinthu zimene Mulungu adakuloleza kuti uchite ndipo iwe ufuna kukondweretsa akazi ako? Ndipo Mulungu ndi wokhululukira nthawi zonse, Mwini chisoni chosatha