29.Zonse zimene zimakhala kumwamba ndi padziko lapansi zimapempha kwa Iye. Tsiku lililonse Iye amakhala ndi chochita
33.oh inu gulu la Majini ndi Anthu! Ngati muli ndi mphamvu zodutsa malire a kumwamba ndi dziko lapansi, dutsani. Komatu inu simungadutse popanda chilolezo
39.Motero patsiku limeneli, sipadzakhala mafunso kuchokera kwa Munthu kapena Majini okhudza machimo awo
54.Iwo adzagona pa makama amene nsalu yake ya m’kati idzakhala yasilika ndipo zipatso za m’minda iwiriyi zidzakhala pafupi pawo
56.M’menemo mudzakhala wodzisunga ndi ogwetsa nkhope zawo pansi amene Munthu kapena Majini sadawakhudze