الحاج یوسف محمد کنیمولا · chiCheŵa, chinyanja

1.Kuyamikidwa konse ndi kwa Mulungu, Namalenga wakumwamba ndi dziko lapansi, amene adalenga angelo, atumwi ouluka, amapiko awiri, atatu ndi anayi. Iye amachulukitsa zolengedwa mwachifuniro chake. Ndithudi Mulungu ali ndi mphamvu pa chinthu china chilichonse