الحاج یوسف محمد کنیمولا · chiCheŵa, chinyanja

1.Kuyamikidwa konse ndi kwa Mulungu Mwini wa chilichonse chakumwamba ndi dziko lapansi ndipo kuyamikidwa konse ndi kwake m’dziko limene lili nkudza. Ndipo Iye ndi waluntha ndi wozindikira