اخلاص
الحاج یوسف محمد کنیمولا · chiCheŵa, chinyanja
1.
Nena: Iye ndi Mulungu, mmodzi
2.
Mulungu, Mwini Mphamvu zonse
3.
Iye sabereka ndipo Iye sadaberekedwe
4.
Ndipo palibe wina wofanana naye