الحاج يوسف محمد كنيمولا · chiCheŵa, chinyanja

١.Kuyamikidwa konse ndi kwa Mulungu Mwini wa chilichonse chakumwamba ndi dziko lapansi ndipo kuyamikidwa konse ndi kwake m’dziko limene lili nkudza. Ndipo Iye ndi waluntha ndi wozindikira