الحاج يوسف محمد كنيمولا · chiCheŵa, chinyanja

١.Ulemerero ukhale kwa Iye amene adayendetsa kapolo wake nthawi ya usiku kuchoka ku Mzikiti Wolemekezeka kupita ku Mzikiti wakutali umene malo ake ozungulira tidawadalitsa; kuti timuonetse zina za zizindikiro zathu. Ndithudi Iye ndiwakumva ndipo woona zonse