الحاج يوسف محمد كنيمولا · chiCheŵa, chinyanja

١.Alif Lam Ra. Tavumbulutsa Buku lino kwa iwe kuti uwatulutse anthu kuchoka kumdima ndi kupita kowala, kunjira ya Mwini Mphamvu, ndi Mwini kuyamikidwa mwachifuniro cha Ambuye wawo