الفيل
الحاج يوسف محمد كنيمولا · chiCheŵa, chinyanja
١.
Kodi siudaone mmene Mulungu adachitira ndi eni ake a Njovu
٢.
Kodi Iye sadasokoneze chiwembu chawo
٣.
Ndipo anatumiza gulu la mbalame lolimbana nawo
٤.
Zimene zinawalasa miyala ya moto
٥.
Ndipo iwo adaoneka ngati msipu wodyedwa