8.Iwo analibe mlandu wina uliwonse ndi anthuwa kupatula kuti anali kukhulupirira mwa Mulungu mmodzi yekha, Mwini mphamvu zonse, Mwini kuyamikidwa
10.Ndithudi onse amene adazunza amuna okhulupirira, ndi akazi okhulupilira ndipo salapa machimo awo, adzalandira chilango chowawa cha moto woyaka wa ku Gahena
11.Ndithu onse amene akhulupirira ndi kuchita ntchito zabwino adzakhala m’minda imene ili ndi mitsinje ya madzi oyenda. Kumeneko ndiko kupambana kwakukulu