40.Koma kwa iwo amene amaopa kukaima pamaso pa Ambuye wake ndi machimo ndipo anali kudziletsa kuchita chifuniro chopanda pake
46.Patsiku limene iwo adzachiona chigumula, kudzakhala ngati kuti iwo sanakhale padziko lapansi nthawi yaitali koma usiku umodzi kapena usana wokha