الحاج یوسف محمد کنیمولا · chiCheŵa, chinyanja

1.Pamene anthu a chinyengo amadza kwa iwe amati: “Ife tichitira umboni kuti iwe, ndithudi, ndiwe Mtumwi wa Mulungu. Inde Mulungu amadziwa kuti iwe, ndithudi, ndiwe Mtumwi wake ndipo Mulungu achitira umboni kuti anthu achinyengo, ndithudi, ndi abodza