10.Ndipo gulu la iwo amene adzakhala kutsogolo m’chikhulupiriro adzakhala kutsogolo m’moyo umene uli nkudza
47.Ndipo iwo anali kukonda kunena kuti: “Pamene ife tafa ndi kusanduka fumbi ndi mafupa, kodi tingadzaukitsidwenso?”
70.Chikadakhala chifuniro chathu tikadawapanga iwo kukhala a mchere. Nanga ndi chifukwa chiyani simuthokoza
83.Nanga ndi chifukwa chiyani inu simuthandiza pamene mzimu wa munthu amene ali kufa ufika pa khosi pake