۴.Angelo ndi Mzimu amakwera kupita kwa Iye mtsiku limodzi limene lingafanizidwe ndi zaka zikwi makumi asanu
۱۱.Iwo azidzawaona iwo. Munthu wochita zoipa adzafunitsitsa kuti mwina akhoza kudzipulumutsa ku chilango cha tsikuli popereka ana ake
۴۲.Motero asiye ayambe adzinyenga ndi chisangalalo mpaka pamene adzakumana ndi tsiku lawo limene adalonjezedwa
۴۳.Tsiku limene adzatuluka mwansanga m’manda mwawo ngati anthu a pa mpikisano umene amalandirirapo mphotho
۴۴.Atayang’ana maso awo pansi ndipo adzachititsidwa manyazi. Limeneli ndilo tsiku limene analonjezedwa