الحاج يوسف محمد كنيمولا · chiCheŵa, chinyanja

١.Oh iwe Mtumwi! Bwanji ukudziletsa zinthu zimene Mulungu adakuloleza kuti uchite ndipo iwe ufuna kukondweretsa akazi ako? Ndipo Mulungu ndi wokhululukira nthawi zonse, Mwini chisoni chosatha